Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 61:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndikakonzere iwo amene alira maliro m'Ziyoni, ndi kuwapatsa cobvala kokometsa m'malo mwa phulusa, mafuta akukondwa m'malo mwa maliro, cobvala ca matamando m'malo mwa mzimu wopsinjika; kuti iwo achedwe mitengo ya cilungamo yakuioka Yehova, kuti Iye alemekezedwe.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 61

Onani Yesaya 61:3 nkhani