Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 61:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mzimu wa Ambuye Yehova uli pa ine; pakuti Yehova wandidzoza ine ndilalikire mau abwino kwa ofatsa; Iye wanditumiza ndikamange osweka mtima, ndikalalikire kwa am'nsinga mamasulidwe, ndi kwa omangidwakutsegulidwa kwa m'ndende;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 61

Onani Yesaya 61:1 nkhani