Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 60:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Dzuwa silidzakhalanso kuunika kwako usana, ngakhale mwezi sudzakuunikiranso kuti kuyere; koma Yehova adzakhala kwa iwe kuunika kosatha, ndi Mulungu wako adzakhala ulemerero wako.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 60

Onani Yesaya 60:19 nkhani