Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 60:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ulemerero wa Lebano udzafika kwa iwe; mtengo wamlombwa, mtengo wamkuyu ndi mtengo wanaphini pamodzi, kukometsera malo a kacisi wanga; ndipo ndidzacititsa malo a mapazi anga ulemerero.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 60

Onani Yesaya 60:13 nkhani