Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 6:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo likatsala limodzi la magawo khumi m'menemo, lidzadyedwanso; monga kacere, ndi monganso thundu, imene tsinde lace likhalabe ataigwetsa; cotero mbeu yopatulika ndiyo tsinde lace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 6

Onani Yesaya 6:13 nkhani