Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 58:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi si ndiko kupatsa cakudya cako kwa anjala, ndi kuti ubwere nao kunyumba kwako aumphawi otayika? pakuona wamalisece kuti umbveke, ndi kuti usadzibisire wekha a cibale cako?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 58

Onani Yesaya 58:7 nkhani