Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 58:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi kusala kudya koteroko ndiko ndinakusankha? tsiku lakubvutitsa munthu moyo wace? Kodi ndiko kuweramitsa mutu wace monga bango, ndi kuyala ciguduli ndi phulusa pansi pace? Kodi uyesa kumeneko kusala kudya, ndi tsiku lobvomerezeka kwa Yehova?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 58

Onani Yesaya 58:5 nkhani