Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 58:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ukaletsa phazi lako pa Sabata, ndi kusiya kucita kukondwerera kwako tsiku: langa lopatulika, ndi kuyesa Sabata tsiku lokondwa lopatulika la Yehova, lolemekezeka, ndipo ukalilemekeza ilo, osacita njira zako zokha, osafuna kukondwa kwako kokha, osalankhula mau ako okha;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 58

Onani Yesaya 58:13 nkhani