Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 58:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo Yehova adzakutsogolera posalekai, ndi kukhutitsa moyo wako m'cirala, ndi kulimbitsa mafupa ako; ndipo udzafanana ndi munda wothirira madzi, ndi kasupe wamadzi amene madzi ace saphwa konse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 58

Onani Yesaya 58:11 nkhani