Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 57:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndilenga cipatso ca milomo, Mtendere, mtendere kwa iye amene ali kutari, ndi kwa iye amene ali cifupi, ati Yehova; ndipo ndidzamciritsa iye.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 57

Onani Yesaya 57:19 nkhani