Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 57:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti atero Iye amene ali wamtari wotukulidwa, amene akhala mwacikhalire, amene dzina lace ndiye Woyera, Ndikhala m'malo atari ndi oyera, pamodzi ndi yense amene ali wa mzimu wosweka ndi wodzicepetsa, kutsitsimutsa mzimu wa odzicepetsa, ndi kutsitsimutsa mtima wa osweka.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 57

Onani Yesaya 57:15 nkhani