Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 57:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene pakupfuula iwe akupulumutse amene unawasonkhanitsa; koma mphepo idzawatenga, mpweya udzacotsa onse; koma iye amene andikhulupirira Ine adzakhala ndi dziko, nadzakhala naco colowa m'phiri langa lopatulika.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 57

Onani Yesaya 57:13 nkhani