Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 55:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona, iwe udzaitana mtundu umene sunaudziwa, ndi mtundu umene sunakudziwa udzakuthamangira, cifukwa ca Yehova Mulungu wako, ndi cifukwa ca Woyera wa Israyeli; pakuti Iye wakukometsa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 55

Onani Yesaya 55:5 nkhani