Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 55:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti monga mvula imagwa pansi ndi matalala, kucokera kumwamba yosabwerera komweko, koma ikhamiza nthaka ndi kuibalitsa, ndi kuiphukitsa, ndi kuipatsitsa mbeu kwa wobzyala, ndi cakudya kwa wakudya;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 55

Onani Yesaya 55:10 nkhani