Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 54:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usaope, pakuti sudzakhala ndi manyazi; usasokonezedwe, pakuti sudzacitidwa manyazi; pakuti udzaiwala manyazi a ubwana wako, ndi citonzo ca umasiye wako sudzacikumbukiranso.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 54

Onani Yesaya 54:4 nkhani