Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 53:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tonse tasocera ngati nkhosa; tonse tayenda yense m'njira ya mwini yekha; ndipo Yehova anaika pa Iye mphulupulu ya ife tonse.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 53

Onani Yesaya 53:6 nkhani