Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 51:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tukulani maso anu kumwamba, ndipo muyang'ane pansi pa dziko; pakuti kumwamba kudzacoka ngati utsi, ndi dziko lidzatha ngati copfunda, ndipo iwo amene akhala m'menemo adzafa cimodzimodzi; koma cipulumutso canga cidzakhala ku nthawi lonse, ndi cilungamo canga sicidzacotsedwa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 51

Onani Yesaya 51:6 nkhani