Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 51:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndaika mau anga m'kamwa mwako; ndipo ndakuphimba ndi mthunzi wa dzanja langa, kuti ndikhazike kumwamba ndi kuika maziko a dziko lapansi, ndi kunena kwa Ziyoni, Inu ndinu anthu anga.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 51

Onani Yesaya 51:16 nkhani