Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 51:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

waiwala Yehova Mlengi wako, amene anayala m'mwamba, nakhazika maziko a dziko lapansi, ndi kuopabe tsiku lonse cifukwa ca ukali wa wotsendereza, pamene iye akonzeratu kupasula? uli kuti ukali wa wotsendereza?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 51

Onani Yesaya 51:13 nkhani