Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 5:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndidzaupasula; sudzadzomboleredwa kapena kulimidwa; koma padzamera lunguzi ndi minga; ndidzalamuliranso mitambo kuti isabvumbwepo mvula.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 5

Onani Yesaya 5:6 nkhani