Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 49:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzadyetsa iwo amene atsendereza iwe ndi nyama yao yao; ndi mwazi wao wao; iwo adzaledzera monga ndi vinyo wotsekemera; anthu onse adzadziwa kuti Ine Yehova ndiri Mpulumutsi wako, ndi Mombolo wako, Wamphamvu wa Yakobo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 49

Onani Yesaya 49:26 nkhani