Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 49:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nacititsa pakamwa panga ngati lupanga lakuthwa, mu mthunzi wa dzanja lace wandibisa Ine; wandipanga Ine mubvi wotuulidwa; m'phodo mwace Iye wandisungitsa Ine, nati kwa Ine,

Werengani mutu wathunthu Yesaya 49

Onani Yesaya 49:2 nkhani