Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 49:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iwo sadzakhala ndi njala, pena ludzu; ngakhale thukuta, pena dzuwa silidzawatentha; pakuti Iye amene wawacitira cifundo, adzawatsogolera, ngakhale pa akasupe a madzi adzawatsogolera.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 49

Onani Yesaya 49:10 nkhani