Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 48:21-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Ndipo iwo sanamva ludzu, pamene Iye anawatsogolera m'mapululu; anawaturutsira madzi kuturuka m'matanthwe; anadulanso thanthwe, madzi nabulika.

22. 1 Kulibe mtendere, ati Yehova, kwa oipa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 48