Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 47:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Watopa mu uphungu wako wambiri; aimirire tsopano openda zam'mwamba, oyang'ana nyenyezi, akuneneratu mwezi ndi mwezi, ndi kukupulumutsa pa zinthu zimene zidzakugwera.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 47

Onani Yesaya 47:13 nkhani