Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 47:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace coipa cidzafika pa iwe; sudzadziwa kuca kwace, ndipo cionongeko cidzakugwera; sudzatha kucikankhira kumbali; ndipo cipasuko cosacidziwa iwe cidzakugwera mwadzidzidzi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 47

Onani Yesaya 47:11 nkhani