Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 47:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsika, ukhale m'pfumbi, namwaliwe, mwana wamkazi wa Babulo; khala pansi popanda mpando wacifumu, mwana wamkazi wa Akasidi, pakuti iwe sudzayesedwanso wozizira ndi wololopoka.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 47

Onani Yesaya 47:1 nkhani