Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 46:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Beli agwada pansi, Nebo awerama; mafano ao ali pa zoweta, ndi pa ng'ombe; zinthu zimene inu munanyamula ponseponse ziyesedwa mtolo, katundu wakulemetsa nyama.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 46

Onani Yesaya 46:1 nkhani