Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 45:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Igwani pansi, inu m'mwamba, kucokera kumwamba, thambo litsanulire pansi cilungamo; dziko lapansi litseguke, kuti libalitse cipulumutso, nilimeretse cilungamo cimere pamodzi; Ine Yehova ndinacilenga cimeneco.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 45

Onani Yesaya 45:8 nkhani