Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 45:24-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

24. Koma mwa Yehova yekha, wina adzati kwa Ine, muli cilungamo ndi mphamvu; ngakhale kwa Iyeyo anthu adzafika, ndi onse amene anamkwiyira, adzakhala ndi manyazi.

25. Mwa Yehova mbeu yonse ya Israyeli idzalungamitsidwa ndi 7 kudzikuza.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 45