Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 45:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti atero Yehova amene analenga kumwamba, Iye ndiye Mulungu amene anaumba dziko lapansi, nalipanga; Iye analikhazikitsa, sanalilenga mwacabe; Iye analiumba akhalemo anthu; Ine ndine Yehova; ndipo palibenso wina.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 45

Onani Yesaya 45:18 nkhani