Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 45:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova kwa wodzozedwa wace kwa Koresi, amene dzanja lace lamanja ndaligwiritsa, kuti agonjetse mitundu ya anthu pamaso pace, ndipo ndidzamasula m'cuuno mwa mafumu; atsegule zitseko pamaso pace, ndi zipata sizidzatsekedwa:

Werengani mutu wathunthu Yesaya 45

Onani Yesaya 45:1 nkhani