Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 44:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ndidzathira madzi pa dziko limene liribe madzi, ndi mitsinje pa nthaka youma; ndidzathira mzimu wanga pa mbeu yako, ndi mdalitso wanga pa obadwa ako;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 44

Onani Yesaya 44:3 nkhani