Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 44:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndine amene ndilimbitsa mau a mtumiki wanga, kucita uphungu wa amithenga anga; ndi kunena za Yerusalemu, Adzakhalamo anthu; ndi za midzi ya Yuda; Idzamangidwa; ndipo ndidzautsa malo abwinja ace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 44

Onani Yesaya 44:26 nkhani