Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 44:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo cotsalaco apanga mlungu, ngakhale fano lace losema; iye aligwadira, nalipembedza, nalipemphera nati, Ndipulumutse ine, cifukwa kuti ndinu mulungu wanga.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 44

Onani Yesaya 44:17 nkhani