Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 42:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Mulungu Yehova, Iye amene analenga thambo, nalifutukula, nayala ponse dziko lapansi, ndi cimene cituruka m'menemo, Iye amene amapatsa anthu a m'menemo mpweya, ndi mzimu kwa iwo amene ayenda m'menemo;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 42

Onani Yesaya 42:5 nkhani