Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 42:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma awa ndiwo anthu olandidwa zao ndi kufunkhidwa; iwo onse agwa m'mauna, nabisidwa m'nyumba zakaidi; alandidwa zao, palibe wowapulumutsa; afunkhidwa ndipo palibe woti, Bwezerani.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 42

Onani Yesaya 42:22 nkhani