Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 42:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yimbirani Yehova nyimbo yatsopano, ndi matamando ace kucokera ku malekezero a dziko lapansi; inu amene mutsikira kunyanja, ndi zonse ziri m'menemo, zisumbu ndi okhala mommo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 42

Onani Yesaya 42:10 nkhani