Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 41:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usaope, Yakobo, nyongolotsi iwe, ndi anthu inu a Israyeli; ndidzakuthangata iwe, ati Yehova, ndiye Mombolo wako, Woyera wa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 41

Onani Yesaya 41:14 nkhani