Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 40:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma iwo amene alindira Yehova adzatenganso mphamvu; adzauluka pamwamba ndi mapiko monga ziombankhanga; adzathamanga kuma osalema; adzayenda koma osalefuka.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 40

Onani Yesaya 40:31 nkhani