Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 40:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Iye amene akhala pamwamba pa malekerezo a dziko lapansi, ndipo okhalamo akunga ziwala; amene afutukula thambo ngati cinsaru, naliyala monga hema wakukhalamo;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 40

Onani Yesaya 40:22 nkhani