Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 37:38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo panali, pamene iye analikupembedzera m'nyumba ya Nisiroki, mulungu wace, Adrameleki ndi Sarezeri, ana ace anampha iye ndi lupanga; ndipo iwo anapulumuka, nathawira ku dziko la ku Ararati. Ndipo Esaradoni, mwana wace, analamulira m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 37

Onani Yesaya 37:38 nkhani