Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 37:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Wamtonza Ambuye ndi atumiki ako, ndipo wati, Ndi khamu la magareta anga ine ndafika ku nsonga za mapiri, ku mbali za Lebano; ndipo ndidzagwetsapo mikungudza yaitali, ndi milombwa yosankhika; ndipo ine ndidzafika pamutu pace penipeni, ku nkhalango ya munda wace wobalitsa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 37

Onani Yesaya 37:24 nkhani