Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 34:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Lupanga la Yehova lakhuta ndi mwazi, lanona ndi mafuta ndi mwazi wa ana a nkhosa, ndi mbuzi, ndi mafuta a imso ya nkhosa zamphongo; pakuti Yehova ali ndi nsembe m'Bozira, ndi ophedwa ambiri m'dziko la Edomu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 34

Onani Yesaya 34:6 nkhani