Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 34:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Funani inu m'buku la Yehova, nimuwerenge; palibe umodzi wa iye udzasowa, palibe umodzi udzasowa unzace; pakuti pakamwa pa Yehova panena, ndipo mzimu wace wasonkhanitsa iwo.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 34

Onani Yesaya 34:16 nkhani