Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 33:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tayang'ana pa Ziyoni, mudzi wa mapwando athu; maso ako adzaona Yerusalemu malo a phe, cihema cimene sicidzasunthidwa, ziciri zace sizidzazulidwa konse, zingwe zace sizidzadulidwa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 33

Onani Yesaya 33:20 nkhani