Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 33:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye amene ayenda molungama, nanena molunjika; iye amene anyoza phindu lonyenga, nasansa manja ace kusalandira zokometsera milandu, amene atseka makutu ace kusamva za mwazi, natsinzina maso ace kusayang'ana coipa;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 33

Onani Yesaya 33:15 nkhani