Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 30:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Katundu wa zirombo za kumwera.M'dziko lobvuta ndi lopweteka, kumeneko kucokera mkango waukazi, ndi wamphongo, mphiri, ndi njoka youluka yamoto, iwo anyamula cuma cao pamsana pa aburu, ndi ang'ono zolemera zao pa malinundu a ngamila, kunka kwa anthu amene sadzapindula nao.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 30

Onani Yesaya 30:6 nkhani