Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 30:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova adzamveketsa mau ace a ulemerero, ndipo adzaonetsa kumenya kwa dzanja lace, ndi mkwiyo wace waukali, ndi lawi la moto wonyambita, ndi kuomba kwa mphepo, ndi mkuntho ndi matalala.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 30

Onani Yesaya 30:30 nkhani