Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 30:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi mpweya wace uli ngati mtsinje wosefukira, umene ufikira m'khosi, kupeta mitundu ya anthu ndi copetera ca cionongeko; ndi capakamwa calakwitsa, cidzakhala m'nsagwada za anthu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 30

Onani Yesaya 30:28 nkhani